Warning: Undefined array key "HTTP_ACCEPT_LANGUAGE" in H:\root\home\rubicube-001\www\site3\wp-content\plugins\payment-gateway-for-visa-for-woocommerce\index.php on line 205

Mkango, Fisi ndi Galu

ZK40.00

Author: BUPE A MWANSA

ISBN: 978-9982-24-152-6

Description

Kabuku aka ka ana kanacokera kunyimbo zomwe Mai Nakaunda anali kuzimbira m’madzulo ngati tiri kuceza panyumba tikadali ana ang’ono-ang’ono.

Popeza kuti masiku ano ana ambiri alibe mwai wokhala pamodzi ndi agogo ao akulu-akulu, ndaganiza kuti ncabwino kuti ndilembe kabuku aka kuti aziwerengako ndi kukondweretsedwa ndi nkhani zake ziri mkatimu. Culukitsani polembako nkhani zanu-zanu zotere monga ine ndacita.